Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 18:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo asanathe masikuwo, ananyamuka Davide, ndi anthu ace, nakaphako Afilisti mazana awiri, ndipo Davide anatenga nsonga za makungu ao nazipatsa mofikira kwa mfumu, kuti akhale mkamwini wa mfumu. Ndipo Sauli anampatsa Mikala mwana wace wamkazi akhale mkazi wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 18

Onani 1 Samueli 18:27 nkhani