Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 18:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Sauli, Mudzatero kwa Davide, kuti mfumu safuna colowolera cina, koma nsonga za makungu zana limodzi za Afilisti, kuti abwezere cilango adani a mfumu. Koma Sauli anaganizira kupha Davide ndi dzanja la Afilisti.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 18

Onani 1 Samueli 18:25 nkhani