Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 18:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli anati kwa Davide, Ona, mwana wanga wamkazi wamkuru, dzina lace Merabi, iyeyo ndidzakupatsa akhale mkazi wako; koma undikhalire ngwazi, nuponye nkhondo za Yehova. Pakuti Sauli anati, Dzanja langa lisamkhudze, koma dzanja la Afilisti ndilo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 18

Onani 1 Samueli 18:17 nkhani