Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 17:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akakhoza iyeyo kuponyana ndi ine ndi kundipha, tidzakhala ife akapolo anu; koma ine ndikamlaka, ndi kumupha, tsono mudzakhala inu akapolo athu, ndi kutitumikira ife.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:9 nkhani