Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 17:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anamanga lupanga lace pamwamba pa zobvala zace, nayesa kuyenda nazo; popeza sanaziyesera kale. Ndipo Davide anati kwa Sauli, Sindikhoza kuyenda ndi izi; pakuti sindinazizolowera. Nazibvula Davide.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:39 nkhani