Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 17:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli anati kwa Davide, Sukhoza iwe kukomana ndi Mfilisti uyu kukaponyana naye; pakuti iwe ndiwe mnyamata, koma iye anazolowera nkhondo kuyambira ubwana wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:33 nkhani