Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 17:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eliabu mkuru wace anamumva iye alikulankhula ndi anthu; ndipo Eliabu anapsa mtima ndi Davide, nati, Unatsikiranji kuno? ndi nkhosa zija zowerengeka unazisiya ndi yani, m'cipululu muja? Ine ndidziwa kudzikuza kwako ndi kuipa kwa mtima wako; pakuti watsika kuti udzaone nkhondoyi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:28 nkhani