Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 17:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anauka m'mamawa, nasiyira nkhosa wozisungira, nasenza zija, namuka, monga anamuuza Jese; ndipo iye anafika ku linga la magareta, napeza khamu lirikuturuka kunka poponyanira nkhondo lirikupfuula.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:20 nkhani