Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 17:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Afilisti anasonkhanitsa makamu ao a nkhondo, naunjikana ku Soko wa ku Yuda, namanga zithando pakati pa Soko ndi Azeka ku Efesi-damimu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:1 nkhani