Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 16:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Samueli anatenga nyanga ya mafuta, namdzoza pakati pa abale ace; ndipo mzimu wa Yehova unalimbika pa Davide kuyambira tsiku lomweli. Ndipo Samueli ananyamuka, Danks ku Rama.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 16

Onani 1 Samueli 16:13 nkhani