Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 16:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Samueli anati kwa Jese, Ana anu ndi omwewa kodi? Nati iye, Watsala wina, mng'ono wa onse, ndipo taonani, iye alikuweta nkhosa. Ndipo Samueli anati kwa Jese, Tumiza munthu akamtenge; pakuti ife sitidzakhala pansi kufikira iye atadza kuno.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 16

Onani 1 Samueli 16:11 nkhani