Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 15:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Sauli ndi anthu anamsunga wamoyo Agagi, ndi nkhosa zokometsetsa, ndi ng'ombe, ndi zonenepa zina, ndi ana a nkhosa, ndi zabwino zonse, sadafuna kuzitha psiti; koma zonse zoipa ndi zonyansa anaziononga konse konse.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:9 nkhani