Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 15:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli anauza Akeni kuti, Mukani, cokani mutsike kuturuka pakati pa Aamaleki, kuti ndingakuonongeni pamodzi ndi iwo; pakuti inu munacitira ana a Israyeli onse zabwino, pakufuma iwo ku Aigupto. Comwece Akeni anacoka pakati pa Aamaleki.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:6 nkhani