Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 15:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti kupanduka kuli ngati coipa ca kucita nyanga, ndi mtima waliuma uli ngati kupembedza milungu yacabe ndi maula. Popeza inu munakaniza mau a Yehova, Iyenso anakaniza inu, kuti simudzakhalanso mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:23 nkhani