Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 15:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova wa makamu, Ndinaonerera cimene Amaleki anacitira Israyeli, umo anamlalira panjira, m'mene iye anakwera kuturuka m'Aigupto.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:2 nkhani