Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 14:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Jonatani ananena ndi mnyamata wonyamula zida zace, Tiye tipite ku kaboma ka osadulidwa awa; kapena Yehova adzatigwirira nchito; pakuti palibe comletsa Yehova kupulumutsa angakhale ndi ambiri kapena ndi owerengeka.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:6 nkhani