Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 14:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthuwo ananena ndi Sauli, Kodi Jonatani adzafa, amene anacititsa cipulumutso cacikuru ici m'Israyeli? Musatero. Pali Yehova, palibe tsitsi limodzi la pa mutu wace lidzagwa pansi, pakuti iye anagwirizana ndi Mulungu lero. Comweco anthuwo anapulumutsa Jonatani kuti angafe. Ndipo Sauli analeka kuwapitikitsa Afilistiwo;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:45 nkhani