Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 14:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Sauli ananena ndi Jonatani, Undiuze cimene unacita. Ndipo Jonatani anamuuza, nati, Zoonadi ndinangolawako uci pang'ono ndi nsonga ya ndodo inali m'dzanja langa: ndipo onani ndiyenera kufa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:43 nkhani