Kuwapha koyambako, Jonatani ndi wonyamula zida zace, anapha monga anthu makumi awiri, monga ndime ya munda yolima ng'ombe ziwiri tsiku limodzi.