Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 13:22-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Comweco kunali kuti tsiku lankhondolo sunapezeka mkondo kapena lupanga m'manja a anthu onse anali ndi Sauli ndi Jonatani; koma Sauli yekha ndi Jonatani mwana wace anali nazo.

23. Ndipo a ku kaboma ka Afilisti anaturuka kunka ku mpata wa ku Mikimasi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13