Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 13:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Sauli anadzisankhira anthu zikwi zitatu a Israyeli; zikwi ziwiri za iwowa zinali ndi Sauli ku Mikimasi, ndi ku phiri la ku Beteli; ndi cikwi cimodzi anali ndi Jonatani ku Gibeya wa ku Benjamini; ndipo anawauza anthu ena onse amuke ku mahema ao.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:2 nkhani