Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 13:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo owawanya anaturuka ku zithando za Afilisti magulu atatu; gulu limodzi linalowa njira yonka ku Ofra, ku dera la Sauli;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:17 nkhani