Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 12:24-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Koma mumuope Yehova, ndi kumtumikira koona, ndi mtima wanu wonse; lingalirani zinthu zazikuruzo iye anakucitirani.

25. Koma mukaumirirabe kucita coipa, mudzaonongeka, inu ndi mfumu yanu yomwe.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 12