Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 12:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene munaona kuti Nahasi mfumu ya ana a Amoni inadza kuponyana nanu, munanena ndi ine, Koma mfumu itiweruze; ngakhale mfumu yanu ndiye Yehova Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 12

Onani 1 Samueli 12:12 nkhani