Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 11:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mawa mwace Sauli anagawa anthu magulu atatu; ndipo iwowa anafika pakati pa zithandozo m'ulonda wa mamawa, nakantha Aamoni kufikira kutentha kwa dzuwa. Ndipo otsalawo anabalalika, osatsala pamodzi ngakhale awiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 11

Onani 1 Samueli 11:11 nkhani