Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 11:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Nahasi M-amoni anakwera, namanga Yabezi Gileadi zithando; ndipo anthu onse a ku Yabezi anati kwa Nahasi, Mupangane cipangano ndi ife, ndipo tidzakutumikirani inu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 11

Onani 1 Samueli 11:1 nkhani