Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 10:26-27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

26. Ndi Sauli yemwe anamuka ku nyumba yace ku Gibeya; ndipo am'khamu anatsagana naye iwo amene Mulungu adakhudza mitima yao.

27. Koma oipa ena anati, Uyu adzatipulumutsa bwanji? Ndipo anampeputsa, osakampatsa mtulo. Koma iye anakhala cete.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10