Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 10:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nanena ndi ana a Israyeli, Atero Yehova, Mulungu wa Israyeli kuti, Ine ndinaturutsa Israyeli m'Aigupto, ndipo ndinakupulumutsani m'manja a Aaigupto, ndi m'manja a maufumu onse anakusautsani;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10

Onani 1 Samueli 10:18 nkhani