Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthuyu akakwera caka ndi caka kuturuka m'mudzi mwace kukalambira ndi kupereka nsembe kwa Mulungu wa makamu m'Silo. Ndipo pomwepo panali ana amuna awiri a Eli, ansembe a Yehova, ndiwo Hofeni ndi Pinehasi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1

Onani 1 Samueli 1:3 nkhani