Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 1:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musamandiyesa mdzakazi wanu mkazi woipa; cifukwa kufikira lero ndinalankhula mwa kucuruka kwa kudandaula kwanga ndi kubvutika kwanga.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1

Onani 1 Samueli 1:16 nkhani