Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 5:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu wa Israyeli anautsa mzimu wa Puli mfumu ya Asuri, ndi mzimu wa Tigilati Pilesere mfumu ya Asuri, ndiye anawatenga ndende; ndiwo Arubeni, ndi Agadi, ndi pfuko la Manase logawika pakati, nafika nao ku Hala, ndi Habori, ndi Hara ndi ku mtsinje wa Gozani, mpaka lero lino.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 5

Onani 1 Mbiri 5:26 nkhani