Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 3:3-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. wacisanu Sefatiya wa Abitali, wacisanu ndi cimodzi Itreamu wa mkazi wace Egila,

4. Anambadwira asanu ndi mmodzi m'Hebroni; ndi pomwepo anakhala mfumu zaka zisanu ndi ziwiri, ndi miyezi isanu ndi iwiri; ndi m'Yerusalemu anakhala mfumu zaka makumi atatu mphambu zitatu.

5. Ndipo ombadwira m'Yerusalemu ndi awa: Simeya, ndi Sobabu, ndi Natani, ndi Solomo, anai a Batisuwa mwana wamkazi wa Amieli;

6. ndi Ibara, ndi Elisama, ndi Elifeleti,

7. ndi Noga, ndi Nefegi, ndi Yafiya,

8. ndi Elisama, ndi Eliada, ndi Elifeleti, asanu ndi anai.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 3