Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 3:22-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Ndi mwana wa Sekaniya: Semaya; ndi ana a Semaya: Hatusi, ndi Igali, ndi Bariya, ndi Neariya, ndi Safati; asanu ndi mmodzi.

23. Ndi ana a Neariya: Eliunai, ndi Hizikiya, ndi Azrikamu, atatu.

24. Ndi ana a Eliunai: Hodavia, ndi Eliasibu, ndi Pelaya, ndi Akubu, ndi Yohanana, ndi Delaya, ndi Anani, asanu ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 3