Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 3:11-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Yoramu mwana wace, Ahaziya mwana wace, Yoasi mwana wace,

12. Amaziya mwana wace, Azariya mwana wace, Yotamu mwana wace,

13. Ahazi mwana wace, Hezekiya mwana wace, Manase mwana wace,

14. Amoni mwana wace, Yosiya mwana wace.

15. Ndi ana a Yosiya: woyamba Yohanana, waciwiri Yehoyakimu, wacitatu Zedekiya, wacinai Salumu.

16. Ndi ana a Yehoyakimu: Yekoniya mwana wace, Zedekiya mwana wace.

17. Ndi mwana wa Yekoniya: Asiri, Sealitiyeli mwana wace,

18. ndi Malikiramu, ndi Pedaya, ndi Senazara, Yekamiya, Hosama, Nedabiya.

19. Ndi ana a Pedaya: Zerubabeli, ndi Simei; ndi ana a Zerubabeli: Mesulamu, ndi Hananiya; ndipo Selomiti ndiye mlongo wao,

20. ndi Hasuba, ndi Oheli, ndi Berekiya, ndi Hasadiya, ndi Yusabi-hesedi; asanu.

21. Ndi ana a Hananiya: Pelatiya, ndi Yesaya, ana a Refaya, ana a Arinani, ana a Obadiya, ana a Sekaniya.

22. Ndi mwana wa Sekaniya: Semaya; ndi ana a Semaya: Hatusi, ndi Igali, ndi Bariya, ndi Neariya, ndi Safati; asanu ndi mmodzi.

23. Ndi ana a Neariya: Eliunai, ndi Hizikiya, ndi Azrikamu, atatu.

24. Ndi ana a Eliunai: Hodavia, ndi Eliasibu, ndi Pelaya, ndi Akubu, ndi Yohanana, ndi Delaya, ndi Anani, asanu ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 3