Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 26:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi abale ace ngwazi ndiwo zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi awiri, akuru a nyumba za makolo, amene mfumu Davide anaika akhale oyang'anira a Arubeni, ndi Agadi, ndi pfuko la Manase logawika pakati, pa zinthu zonse za Mulungu ndi zinthu za mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 26

Onani 1 Mbiri 26:32 nkhani