Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 24:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi Semaya mwana wa Netaneli mlembi, ndiye wa Alevi, anawalembera pamaso pa mfumu; ndi akalonga, ndi Zadoki wansembe, ndi Ahimeleke mwana wa Abyatara, a akuru a nyumba za makolo a ansembe ndi Alevi, anatenga nyumba imodzi ya kholo lace ya Eleazara, ndi imodzi ya Itamara.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 24

Onani 1 Mbiri 24:6 nkhani