Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 22:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona tsono, m'kuzunzika kwanga ndinakonzeratu nyumba ya Yehova matalente zikwi zana limodzi a golidi, ndi matalente zikwi zikwi a siliva, ndi mkuwa, ndi citsulo, osayesa kulemera kwace, pakuti zidacurukaeli; mitengo yomwe ndi miyala ndakonzeratu; nuonjezereko.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 22

Onani 1 Mbiri 22:14 nkhani