Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 2:9-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Ndi ana a Hezironi anambadwirawo: Yerameli, ndi Ramu, ndi Kelubai.

10. Ndi Ramu anabala Aminadabu; ndi Aminadabu anabala Nasoni kalonga wa ana a Yuda;

11. ndi Nasoni anabala Salima, ndi Salima anabala Boazi,

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 2