Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 2:49-55 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

49. Iyeyu anabalanso Safa atate wa Madimana, Seva atate wa Makibena, ndi atate wa Gibeya; ndi mwana wamkazi wa Kalebi ndiye Akisa.

50. Ana a Kalebi ndi awa: mwana wa Huri, mwana woyamba wa Efrata, Sobali atate wa Kiriate Yearimu.

51. Salma atate wa Betelehemu, Harefi atate wa Betigaderi.

52. Ndipo Sobali atate wa Kiriati-Yearimu anali ndi ana: Haroe, ndi Hazi Hamenukoti.

53. Ndi mabanja a Kiriati-Yearimu: Aitiri, ndi Aputi, ndi Asumati, ndi Amisrai; Aforati ndi Aestaoli anafuma kwa iwowa.

54. Ana a Salma: Betelehemu, ndi Anetofati, Atroti Beti Yoabu, ndi Hazi Hamanahati, ndi Azori.

55. Ndi mabanja a alembi okhala ku Yabezi: Atirati, Asimeati, Asukati. Iwo ndiwo Akeni ofuma ku Hamati, kholo la nyumba ya Rekabu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 2