Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 2:10-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Ndi Ramu anabala Aminadabu; ndi Aminadabu anabala Nasoni kalonga wa ana a Yuda;

11. ndi Nasoni anabala Salima, ndi Salima anabala Boazi,

12. ndi Boazi anabala Obedi, ndi Obedi anabala Jese,

13. ndi Jese anabala mwana wace wamwamuna woyamba Eliabu, ndi Abinadabu waciwiri, ndi Simeya wacitatu,

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 2