Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 2:1-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ana a Israyeli ndi awa: Rubeni, Simeoni, Levi, ndi Yuda, Isakara, ndi Zebuluni,

2. Dani, Yosefe, ndi Benjamini, Nafitali, Gadi, ndi Aseri.

3. Ana a Yuda ndiwo Eri, ndi Onani, ndi Sela; Batisua Mkanani anambalira atatu amenewa. Koma Eri mwana woyamba wa Yuda anali woipa pamaso pa Yehova, ndi iye anamupha.

4. Ndi Tamari mpongozi wace anambalira Perezi ndi Zera. Ana amuna onse a Yuda ndiwo asanu.

5. Ana a Perezi: Hezironi, ndi Hamuli.

6. Ndi ana a Zera: Zimri, ndi Etani, ndi Hemani, ndi Kalikoli, ndi Dara; onse pamodzi ndi asanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 2