Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 14:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anafunsira kwa Mulungu, kun, Ndikwere kodi kuyambana ndi Afilisti? mudzawapereka m'dzanja langa kodi? Ndipo Yehova anati kwa iye, Kwera, pakuti ndidzawapereka m'dzanja lako.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 14

Onani 1 Mbiri 14:10 nkhani