Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 12:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ena a Manase omwe anapambukira kwa Davide, muja iye anadza ndi Afilisti koponyana nkhondo ndi Sauli, koma sanawathandiza; popeza akalonga a Afilisti, atacita upo, anamuuza acoke, ndi kuti, Adzapambukira kwa mbuye wace Sauli ndi kutisandulikira.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 12

Onani 1 Mbiri 12:19 nkhani