Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 10:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene amuna onse a Israyeli okhala m'cigwamo anaona kuti anathawa, ndi kuti Sauli ndi ana ace adafa, anasiya midzi yao, nathawa; nadza Afilisti, nakhala m'menemo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 10

Onani 1 Mbiri 10:7 nkhani