Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 10:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Afilisti tsono analimbana nkhondo ndi Israyeli; ndipo amuna a Israyeli anathawa pamaso pa Afilisti, nagwa ophedwa pa phiri la Giliboa.

2. Ndipo Afilisti anaumirira kutsata Sauli ndi ana ace, ndi Afilistiwo anawapha Yonatani, ndi Abinadabu, ndi Malikisuwa, ana a Sauli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 10