Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mbiri 1:1-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. ADAMU, Seti, Enosi,

2. Kenani, Mahalaheli, Yaredi,

3. Enoki, Metusela, Lameki,

4. Nowa, Semu, Hamu, ndi Yafeti.

5. Ana a Yafeti: Gomeri, ndi Magogi, ndi Madai, ndi Yavani, ndi Tubala, ndi Meseki, ndi Tirasi.

6. Ndi ana a Gomeri: Asikenazi, Difati, ndi Togarima.

7. Ndi ana a Yavani: Elisa, ndi Tarisisa, Kitimu, ndi Rodanimu.

8. Ana a Hamu: Kusi, ndi Mizraimu, Puti, ndi Kanani.

9. Ndi ana a Kusi: Seba, ndi Havila, ndi Sabita, ndi Rama, ndi Sabteka. Ndi ana a Rama: Seba, ndi Dedani.

10. Ndi Kusi anabala Nimmdi; iye anayamba kukhala wamphamvu pa dziko.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 1