Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 9:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Solomo sanawayesa ana a Israyeli akapolo, koma iwowo anali anthu a nkhondo, ndi anyamata ace, ndi akalonga ace, ndi akazembe ace, ndi oyang'anira magareta ace ndi apakavalo ace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 9

Onani 1 Mafumu 9:22 nkhani