Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:66 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku lacisanu ndi citatu anawauza anthu apite; ndipo iwo anadalitsa mfumu, napita ku mahema ao osekera ndi okondwera mtima cifukwa ca zokoma zonse Yehova anacitira Davide mtumiki wace, ndi Israyeli anthu ace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:66 nkhani