Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akaturuka anthu anu kukayambana nkhondo ndi adani ao, kumene konse inu mudzawatuma, ndipo akapemphera kwa Yehova molunjika ku mudzi uno munausankha Inu, ndi ku nyumba ndamangira dzina lanu;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:44 nkhani