Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma muceukire pemphero la kapolo wanu, ndi pembedzero lace, Yehova Mulungu wanga, kumvera kulira ndi kupempha kwace kumene kapolo wanu apempha pamaso panu lero;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:28 nkhani